KODI MWALANDIRA KALE KATEMERA WA CHOLERA?

Kodi mukuziwa kuti tingathe kugonjetsa matenda a Cholera?

Indeee! Tingathe.... Pitani kuchipatala chilichonse chomwe chilipafupi ndipo kalandireni katemera wa Cholera mwa ulele. Kotero, mudzakhala kuti mwatengapo gawo lalikulu pothana ndi thendayi.

Khalani osogola pokalandira katemera wa Cholera pamodzi ndi banja lanu.

#Yetod

#togetherwecandefeatCholera

#it can start with you today!!

Comments

Popular posts from this blog

Youth Empowerment Towards Development (YETOD) Announces 2025 Annual Youth Conference

COMMUNITY FOUNDATIONS DEVELOPMENT PROJECT

FUND RAISING FOR SCHOOL BLOCK CONSTRUCTION AT MSAWA PRIMARY SCHOOL IN T/A MALANDA, NKHATA-BAY, MALAWI