ESTABLISHMENG OF FRIENDS OF CHINTHECHE
https://chat.whatsapp.com/BSOZYWDhBPu376UyOwGHVg
Youth Empowerment Towards Development (YETOD) ndi Bungwe la achinyamata, limene likugwira ntchito mu Boma la Nkhata-bay komanso liri ndi Office yake ku Chintheche. Bungweri likugwira ntchito ngati Community Foundation kumene chitukuko chimatsogoleredwa ndi eni dela. YETOD ikufuna kukhazikisa gulu la Abale a Chintheche (Friends of Chintheche) limene likumema wina aliyense amene Ali osangalatsidwa kutenga nawo mbali pakubweresa chitukuko ku Chintheche ndi madela ozungulira.
Gululi likuyang'anaso munthu wina aliyense wakufuna kwabwino amene amachokera ku Chintheche ndimadela ake ozungulira, Kapena amakhala muchintheche kapena maiko a kunja kapena dela lina, kuphatikizapo wina aliyense amene ali osangalasidwa kutenga udindo wakubwenzera zabwino kudera. Ngati Mukufuna Kuziwa Zambiri, mokhoza kulowa nawo mugululi, limene liri Friends of Chintheche.

Comments
Post a Comment